-
Numeri 16:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako Mose anauza Kora kuti: “Mawa, iweyo ndi anthu onse amene akukutsatira mukaonekere pamaso pa Yehova. Mukaonekere, iweyo, anthuwo komanso Aroni.
-