Numeri 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako Mose ananyamuka nʼkupita kwa Datani ndi Abiramu, ndipo akulu+ a Isiraeli anapita naye limodzi.
25 Kenako Mose ananyamuka nʼkupita kwa Datani ndi Abiramu, ndipo akulu+ a Isiraeli anapita naye limodzi.