-
Numeri 16:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Atafika anauza gululo kuti: “Chonde, chokani kumatenti a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse, kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha tchimo lawo.”
-