Numeri 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ngati anthuwa angafe mmene anthu onse amafera, ndiponso ngati chilango chawo chingakhale chofanana ndi chimene anthu onse amapatsidwa, ndiye kuti Yehova sananditume.+
29 Ngati anthuwa angafe mmene anthu onse amafera, ndiponso ngati chilango chawo chingakhale chofanana ndi chimene anthu onse amapatsidwa, ndiye kuti Yehova sananditume.+