Numeri 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho iwo pamodzi ndi onse amene anali kumbali yawo analowa mʼManda* ali amoyo. Nthaka inawakwirira, moti iwo anawonongedwa pakati pa mpingo wonse.+
33 Choncho iwo pamodzi ndi onse amene anali kumbali yawo analowa mʼManda* ali amoyo. Nthaka inawakwirira, moti iwo anawonongedwa pakati pa mpingo wonse.+