Numeri 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Uza Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti achotse pamoto zofukizirazo+ chifukwa nʼzopatulika. Umuuzenso kuti amwaze motowo kutali.
37 “Uza Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti achotse pamoto zofukizirazo+ chifukwa nʼzopatulika. Umuuzenso kuti amwaze motowo kutali.