Numeri 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndodozo uziike mʼchihema chokumanako, patsogolo pa Umboni,+ pamene ndimakumana nawe nthawi zonse.+