-
Numeri 17:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho Mose analankhula ndi Aisiraeli ndipo atsogoleri awo onse anapereka ndodo zawo. Mtsogoleri aliyense anapereka ndodo imodzi ya fuko lake. Panali ndodo 12, ndipo imodzi inali ya Aroni.
-