Numeri 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Bwezera ndodo ya Aroni+ patsogolo pa Umboni. Uisunge kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana opandukawa,+ nʼcholinga chakuti asiye kungʼungʼudza motsutsana ndi ine komanso kuti asafe.”
10 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Bwezera ndodo ya Aroni+ patsogolo pa Umboni. Uisunge kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana opandukawa,+ nʼcholinga chakuti asiye kungʼungʼudza motsutsana ndi ine komanso kuti asafe.”