Numeri 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zipatso zonse zoyamba kupsa mʼminda yawo, zimene azizipereka kwa Yehova zizikhala zako.+ Aliyense wamʼnyumba yako amene si wodetsedwa angathe kudya nawo.
13 Zipatso zonse zoyamba kupsa mʼminda yawo, zimene azizipereka kwa Yehova zizikhala zako.+ Aliyense wamʼnyumba yako amene si wodetsedwa angathe kudya nawo.