Numeri 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako. Ngati mmene umachitira ndi chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku komanso mwendo wamʼmbuyo wakumanja, nyamayi izikhala yako.+
18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako. Ngati mmene umachitira ndi chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku komanso mwendo wamʼmbuyo wakumanja, nyamayi izikhala yako.+