Numeri 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ine ndapereka kwa ana a Levi chakhumi chilichonse+ mu Isiraeli kuti chikhale cholowa chawo chifukwa cha utumiki umene akuchita, utumiki wapachihema chokumanako. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:21 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 170
21 Ine ndapereka kwa ana a Levi chakhumi chilichonse+ mu Isiraeli kuti chikhale cholowa chawo chifukwa cha utumiki umene akuchita, utumiki wapachihema chokumanako.