-
Numeri 18:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Mukamachita zimenezi inunso muzikhala kuti mwapereka chopereka chanu kwa Yehova, kuchokera pa zakhumi zonse zimene muzilandira kuchokera kwa Aisiraeli. Kuchokera pa zakhumizo, muzipereka chopereka chanu kwa Yehova popereka kwa Aroni wansembe.
-