Numeri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wansembeyo atenge mtengo wa mkungudza, kamtengo ka hisope+ ndi ulusi wofiira kwambiri nʼkuziponya pamoto umene akuwotcherapo ngʼombeyo.
6 Wansembeyo atenge mtengo wa mkungudza, kamtengo ka hisope+ ndi ulusi wofiira kwambiri nʼkuziponya pamoto umene akuwotcherapo ngʼombeyo.