Numeri 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu amene anawotcha ngʼombeyo achape zovala zake nʼkusamba* ndi madzi, ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.
8 Munthu amene anawotcha ngʼombeyo achape zovala zake nʼkusamba* ndi madzi, ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.