Numeri 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu amene wawola phulusa la ngʼombeyo azichapa zovala zake ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kwa Aisiraeli komanso kwa mlendo wokhala pakati pawo.+
10 Munthu amene wawola phulusa la ngʼombeyo azichapa zovala zake ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kwa Aisiraeli komanso kwa mlendo wokhala pakati pawo.+