Numeri 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Gulu lonse la anthuwo litaona kuti Aroni wamwalira, nyumba yonse ya Isiraeli inalira maliro a Aroni kwa masiku 30.+
29 Gulu lonse la anthuwo litaona kuti Aroni wamwalira, nyumba yonse ya Isiraeli inalira maliro a Aroni kwa masiku 30.+