Numeri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo Amowabu anachita mantha kwambiri ndi anthuwo chifukwa anali ambiri. Iwo anagwidwa mantha aakulu chifukwa cha Aisiraeliwo.+
3 ndipo Amowabu anachita mantha kwambiri ndi anthuwo chifukwa anali ambiri. Iwo anagwidwa mantha aakulu chifukwa cha Aisiraeliwo.+