Numeri 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Andanda kukafika kutali ngati zigwa,*+Ngati minda mʼmphepete mwa mtsinje.Ngati mitengo ya aloye imene Yehova anadzala,Ngati mikungudza mʼmbali mwa madzi. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:6 Nsanja ya Olonda,2/1/2014, tsa. 10
6 Andanda kukafika kutali ngati zigwa,*+Ngati minda mʼmphepete mwa mtsinje.Ngati mitengo ya aloye imene Yehova anadzala,Ngati mikungudza mʼmbali mwa madzi.