Numeri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,Ndipo mbewu* yake yadzalidwa mʼmbali mwa madzi ambiri.+ Mfumu yakenso+ idzakhala yamphamvu kuposa Agagi,+Ndipo ufumu wake udzakwezedwa.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:7 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 5
7 Madzi odzaza mitsuko yake iwiri akutayikirabe pansi,Ndipo mbewu* yake yadzalidwa mʼmbali mwa madzi ambiri.+ Mfumu yakenso+ idzakhala yamphamvu kuposa Agagi,+Ndipo ufumu wake udzakwezedwa.+