Numeri 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Limeneli likhala pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake+ ndiponso anaphimba machimo a Aisiraeli.’”
13 Limeneli likhala pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake+ ndiponso anaphimba machimo a Aisiraeli.’”