Numeri 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Muwerenge amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa gulu lonse la Aisiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, potengera nyumba za makolo awo.”+
2 “Muwerenge amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa gulu lonse la Aisiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, potengera nyumba za makolo awo.”+