Numeri 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Muwerenge Aisiraeli onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.”+ Ana a Isiraeli amene anatuluka mʼdziko la Iguputo anali awa:
4 “Muwerenge Aisiraeli onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.”+ Ana a Isiraeli amene anatuluka mʼdziko la Iguputo anali awa: