Numeri 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana aamuna a Gadi+ potengera mabanja awo anali awa: Zefoni amene anali kholo la banja la Azefoni, Hagi amene anali kholo la banja la Ahagi, Suni amene anali kholo la banja la Asuni,
15 Ana aamuna a Gadi+ potengera mabanja awo anali awa: Zefoni amene anali kholo la banja la Azefoni, Hagi amene anali kholo la banja la Ahagi, Suni amene anali kholo la banja la Asuni,