Numeri 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ana aamuna a Zebuloni+ anali awa: Seredi amene anali kholo la banja la Aseredi, Eloni amene anali kholo la banja la Aeloni ndi Yahaleeli amene anali kholo la banja la Ayahaleeli.
26 Ana aamuna a Zebuloni+ anali awa: Seredi amene anali kholo la banja la Aseredi, Eloni amene anali kholo la banja la Aeloni ndi Yahaleeli amene anali kholo la banja la Ayahaleeli.