Numeri 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amenewa anali mabanja a anthu a fuko la Zebuloni. Amuna onse amene anawerengedwa analipo 60,500.+