Numeri 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Tselofekadi, mwana wamwamuna wa Heferi, analibe ana aamuna koma aakazi okhaokha.+ Mayina a ana aakazi a Tselofekadi+ anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.
33 Koma Tselofekadi, mwana wamwamuna wa Heferi, analibe ana aamuna koma aakazi okhaokha.+ Mayina a ana aakazi a Tselofekadi+ anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.