Numeri 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Amenewa anali mabanja a ana a Efuraimu. Amuna onse amene anawerengedwa analipo 32,500.+ Awa anali ana aamuna a Yosefe potengera mabanja awo.
37 Amenewa anali mabanja a ana a Efuraimu. Amuna onse amene anawerengedwa analipo 32,500.+ Awa anali ana aamuna a Yosefe potengera mabanja awo.