Numeri 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ana aamuna a Bela anali Aridi ndi Namani.+ Aridi anali kholo la banja la Aaridi. Namani anali kholo la banja la Anamani.
40 Ana aamuna a Bela anali Aridi ndi Namani.+ Aridi anali kholo la banja la Aaridi. Namani anali kholo la banja la Anamani.