Numeri 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Tsopano awa ndi mayina a amuna amene anawerengedwa pakati pa Alevi+ potengera mabanja awo: Agerisoni, a banja la Gerisoni, Akohati, a banja la Kohati+ ndi Amerari, a banja la Merari.
57 Tsopano awa ndi mayina a amuna amene anawerengedwa pakati pa Alevi+ potengera mabanja awo: Agerisoni, a banja la Gerisoni, Akohati, a banja la Kohati+ ndi Amerari, a banja la Merari.