Numeri 26:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Mabanja a Alevi ndi awa: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi+ ndi banja la Akora.+ Kohati anabereka Amuramu.+
58 Mabanja a Alevi ndi awa: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi+ ndi banja la Akora.+ Kohati anabereka Amuramu.+