Numeri 26:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Onse amene anawerengedwa pakati pa Alevi analipo 23,000. Amenewa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita mʼtsogolo.+ Iwo sanawerengedwe limodzi ndi Aisiraeli,+ chifukwa sanafunikire kulandira cholowa pakati pa Aisiraeli.+
62 Onse amene anawerengedwa pakati pa Alevi analipo 23,000. Amenewa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita mʼtsogolo.+ Iwo sanawerengedwe limodzi ndi Aisiraeli,+ chifukwa sanafunikire kulandira cholowa pakati pa Aisiraeli.+