-
Numeri 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ngati bambo ake alibe azichimwene awo, muzipereka cholowa chake kwa wachibale wake wapafupi wa ku banja lawo, ndipo azitenga cholowacho kuti chikhale chake. Chigamulo chimenechi chidzakhala lamulo kwa Aisiraeli, mogwirizana ndi zimene Yehova walamula Mose.’”
-