Numeri 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako umuimiritse pamaso pa wansembe Eleazara komanso pamaso pa gulu lonse, ndipo umuike kuti akhale mtsogoleri pamaso pawo.+
19 Kenako umuimiritse pamaso pa wansembe Eleazara komanso pamaso pa gulu lonse, ndipo umuike kuti akhale mtsogoleri pamaso pawo.+