-
Numeri 27:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho Mose anachitadi mogwirizana ndi zimene Yehova anamulamula. Anatenga Yoswa nʼkumuimiritsa pamaso pa wansembe Eleazara komanso pamaso pa gulu lonselo.
-