-
Numeri 29:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Muziperekanso nsembe zake zambewu za ufa wosalala wothira mafuta. Popereka ngʼombe yamphongoyo muziperekanso ufa wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Popereka nkhosa yamphongoyo muziperekanso ufa wokwana magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa.
-