-
Numeri 29:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Muziperekanso nsembe zake zambewu za ufa wosalala wothira mafuta. Iliyonse ya ngʼombe 13 zamphongozo muziiperekera ufa wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Iliyonse ya nkhosa zamphongo ziwirizo muziiperekera ufa wokwana magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa.
-