Numeri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muziperekanso mbuzi yaingʼono imodzi monga nsembe yamachimo. Muziipereka kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku ndi nsembe yake yambewu, limodzi ndi nsembe zake zachakumwa.+
19 Muziperekanso mbuzi yaingʼono imodzi monga nsembe yamachimo. Muziipereka kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku ndi nsembe yake yambewu, limodzi ndi nsembe zake zachakumwa.+