Numeri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa tsiku lachitatu, muzipereka ngʼombe 11 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+
20 Pa tsiku lachitatu, muzipereka ngʼombe 11 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+