Numeri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pa tsiku la 6, muzipereka ngʼombe 8 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+
29 Pa tsiku la 6, muzipereka ngʼombe 8 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, zonse zizikhala zopanda chilema.+