Numeri 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pa tsiku la 8, muzichita msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.+