39 Muzipereka zimenezi kwa Yehova pa zikondwerero zanu,+ kuwonjezera pa nsembe zimene mukupereka chifukwa cha lonjezo limene munapanga,+ nsembe zanu zaufulu+ zimene mumapereka kuti zikhale nsembe zanu zopsereza,+ nsembe zanu zambewu,+ nsembe zanu zachakumwa+ ndi nsembe zanu zamgwirizano.’”+