-
Numeri 30:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pa nkhani yokhudza lonjezo lililonse kapena lumbiro lokhudza kudzimana kapenanso kulolera kuvutika, mwamuna wake ali ndi mphamvu zovomereza kapena kukana kuti mkaziyo akwaniritse lonjezolo.
-