-
Numeri 30:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ngati mwamunayo sanatsutse zimene mkazi wakeyo walonjeza, masiku nʼkumapita, ndiye kuti mwamunayo wavomereza malonjezo onse a mkaziyo kapena malumbiro onse odzimana amene mkaziyo anachita. Iye wavomereza chifukwa sanamukanize mkaziyo pa tsiku limene anamva akulonjeza.
-