-
Numeri 30:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Awa ndi malamulo amene Yehova anapatsa Mose okhudza mwamuna ndi mkazi wake, ndiponso bambo ndi mwana wake wachitsikana amene akukhala mʼnyumba mwake.”
-