Numeri 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Mose analankhula ndi anthuwo kuti: “Konzekeretsani amuna pakati panu kuti apite kukamenyana* ndi Amidiyani, ndipo mukapereke chilango cha Yehova kwa Amidiyaniwo pobwezera zimene anachita.
3 Choncho Mose analankhula ndi anthuwo kuti: “Konzekeretsani amuna pakati panu kuti apite kukamenyana* ndi Amidiyani, ndipo mukapereke chilango cha Yehova kwa Amidiyaniwo pobwezera zimene anachita.