-
Numeri 31:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma Aisiraeli anagwira akazi a Chimidiyani ndi ana awo nʼkuwatenga kupita nawo kwawo. Anatenganso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse.
-