Numeri 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mizinda yawo yonse imene ankakhala komanso misasa yawo yonse* anaiwotcha ndi moto.