Numeri 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anatenga anthu amene anawagwirawo limodzi ndi zinthu zina zonse nʼkupita nawo kwa Mose, wansembe Eleazara ndi kugulu la Aisiraeli, kumsasa wawo umene unali mʼchipululu cha Mowabu,+ pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, ku Yeriko.
12 Kenako anatenga anthu amene anawagwirawo limodzi ndi zinthu zina zonse nʼkupita nawo kwa Mose, wansembe Eleazara ndi kugulu la Aisiraeli, kumsasa wawo umene unali mʼchipululu cha Mowabu,+ pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, ku Yeriko.