-
Numeri 31:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Tsopano wansembe Eleazara anauza asilikali amene anapita kunkhondo aja kuti: “Tamverani zimene Yehova analamula Mose,
-